-
Ezekieli 18:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Iye amapewa kupondereza munthu wosauka, sakongoza zinthu mwa katapira ndipo sauza anthu kuti apereke chiwongoladzanja. Amatsatira zigamulo zanga komanso kuyenda motsatira malamulo anga. Munthu wotere sadzafa chifukwa cha zolakwa za bambo ake. Iye adzapitiriza kukhala ndi moyo ndithu.
-