Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 19:5, 6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kenako anagona pansi pa kamtengo kaja mpaka tulo tinamʼpeza. Mwadzidzidzi kunabwera mngelo ndipo anamukhudza+ nʼkumuuza kuti: “Dzuka udye.”+ 6 Atayangʼana, anaona kuti kumutu kwake kuli mkate wozungulira pamiyala yotentha komanso jagi* ya madzi. Eliya anadya nʼkumwa ndipo anagonanso.

  • Salimo 34:9, 10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Opani Yehova, inu oyera ake onse,

      Chifukwa onse amene amamuopa sasowa kanthu.+

      כ [Kaph]

      10 Ngakhale mikango yamphamvu* ingakhale ndi njala chifukwa chosowa chakudya.

      Koma anthu amene akufunafuna Yehova sadzasowa chilichonse chabwino.+

  • Yesaya 65:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti:

      “Atumiki anga adzadya, koma inu mudzakhala ndi njala.+

      Atumiki anga adzamwa,+ koma inu mudzakhala ndi ludzu.

      Atumiki anga adzasangalala,+ koma inu mudzachita manyazi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena