20 Pa tsiku limenelo ndidzaitana mtumiki wanga Eliyakimu,+ mwana wa Hilikiya. 21 Iyeyo ndidzamuveka mkanjo wako ndipo lamba wako ndidzamumanga mwamphamvu mʼchiuno mwake.+ Ulamuliro wako ndidzaupereka mʼmanja mwake ndipo iye adzakhala tate wa anthu okhala mu Yerusalemu ndi amʼnyumba ya Yuda.