Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 18:36, 37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Koma anthuwo anangokhala chete osamuyankha chilichonse, chifukwa mfumu inawalamula kuti: “Musakamuyankhe.”+ 37 Koma Eliyakimu mwana wa Hilikiya amene ankayangʼanira banja lachifumu, Sebina mlembi ndi Yowa mwana wa Asafu wolemba zochitika, anapita kwa Hezekiya atangʼamba zovala zawo ndipo anamuuza zomwe Rabisake ananena.

  • Miyambo 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Amene amalangiza wonyoza amachititsidwa manyazi,+

      Ndipo aliyense wodzudzula woipa adzavulazidwa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena