Yesaya 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Pita kwa Sebina,+ kapitawo woyangʼanira nyumba ya mfumu, ndipo ukamuuze kuti,
15 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Pita kwa Sebina,+ kapitawo woyangʼanira nyumba ya mfumu, ndipo ukamuuze kuti,