Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 35:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Kumeneko kudzakhala msewu waukulu+

      Inde msewu umene udzatchedwe Msewu Wopatulika.

      Munthu wodetsedwa sadzayenda mumsewu umenewo.+

      Amene adzayendemo ndi munthu yekhayo amene ali woyenerera.

      Palibe munthu wopusa amene adzayende mumsewu umenewo.

  • Yesaya 57:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndiyeno wina adzanena kuti, ‘Konzani msewu! Konzani msewu! Konzani njira!+

      Chotsani chopinga chilichonse panjira ya anthu anga.’”

  • Malaki 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Taonani! Ine ndikutumiza mthenga wanga ndipo adzandikonzera njira.+ Mwadzidzidzi, Ambuye woona, amene anthu inu mukumufunafuna, adzabwera kukachisi wake.+ Ndiponso mthenga wa pangano amene mukumuyembekezera mosangalala adzabwera. Iye adzabwera ndithu,” watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena