-
Yesaya 49:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndiyeno iye anati: “Sikuti wangokhala mtumiki wanga
Kuti ubwezeretse mafuko a Yakobo
Ndiponso kuti Aisiraeli amene ali otetezeka uwabwezere kwawo.
-