Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Yehova wanena kuti: “Ngati ungabwerere, iwe Isiraeli,

      Ngati ungabwerere kwa ine

      Ndipo ngati ungachotse mafano ako onyansa pamaso panga,

      Sudzakhalanso moyo wothawathawa.+

  • Ezekieli 33:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Auze kuti, ‘“Pali ine Mulungu wamoyo,” akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, “Ine sindisangalala ndi imfa ya munthu woipa,+ koma ndimafuna kuti munthu woipa asinthe zochita zake+ nʼkupitiriza kukhala ndi moyo.+ Bwererani! Bwererani nʼkusiya zinthu zoipa zimene mukuchita.+ Muferenji inu a nyumba ya Isiraeli?”’+

  • Hoseya 14:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Inu Aisiraeli, bwererani kwa Yehova Mulungu wanu,+

      Popeza mwapunthwa chifukwa cha zolakwa zanu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena