Yeremiya 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzapatsa nkhosazo abusa amene adzaziwete moyenerera.+ Sizidzaopanso kanthu kapena kuchita mantha ndipo palibe imene idzasowe,” akutero Yehova. Ezekieli 34:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndidzazipatsa mʼbusa mmodzi+ amene ndi mtumiki wanga Davide,+ ndipo adzazidyetsa. Iye adzakhala mʼbusa wawo ndipo azidzazidyetsa.+
4 Ndidzapatsa nkhosazo abusa amene adzaziwete moyenerera.+ Sizidzaopanso kanthu kapena kuchita mantha ndipo palibe imene idzasowe,” akutero Yehova.
23 Ndidzazipatsa mʼbusa mmodzi+ amene ndi mtumiki wanga Davide,+ ndipo adzazidyetsa. Iye adzakhala mʼbusa wawo ndipo azidzazidyetsa.+