Ezekieli 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa tsiku limenelo ndinalumbira kuti ndidzawatulutsa mʼdziko la Iguputo nʼkupita nawo kudziko limene ndinawasankhira,* dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Linali dziko lokongola kwambiri kuposa mayiko onse.
6 Pa tsiku limenelo ndinalumbira kuti ndidzawatulutsa mʼdziko la Iguputo nʼkupita nawo kudziko limene ndinawasankhira,* dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Linali dziko lokongola kwambiri kuposa mayiko onse.