Yeremiya 39:11, 12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mfumu Nebukadinezara* ya Babulo inapereka lamulo kwa Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu lokhudza Yeremiya kuti: 12 “Mutenge uzimuyangʼanira ndipo usamuchitire choipa chilichonse. Koma uzimupatsa chilichonse chimene iye wapempha.”+
11 Mfumu Nebukadinezara* ya Babulo inapereka lamulo kwa Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu lokhudza Yeremiya kuti: 12 “Mutenge uzimuyangʼanira ndipo usamuchitire choipa chilichonse. Koma uzimupatsa chilichonse chimene iye wapempha.”+