Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 ‘Kodi Isiraeli ndi mtumiki wanga kapena ndi kapolo wobadwira mʼnyumba mwanga?

      Nanga nʼchifukwa chiyani anthu anamugwira nʼkupita naye kudziko lina?

  • Yeremiya 2:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Anthu a ku Nofi*+ ndi ku Tahapanesi+ anawononga dziko lako.*

  • Yeremiya 44:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Mulungu anauza Yeremiya uthenga woti akauze Ayuda onse amene ankakhala mʼdziko la Iguputo,+ mʼmadera a Migidoli,+ Tahapanesi,+ Nofi*+ ndi Patirosi.+ Uthengawo unali wakuti:

  • Ezekieli 30:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Lupanga lidzabwera kudzaukira Iguputo, ndipo anthu a ku Itiyopiya adzachita mantha kwambiri anthu akadzaphedwa ku Iguputo.

      Chuma cha Iguputo chidzalandidwa ndipo maziko ake adzagwetsedwa.+

  • Ezekieli 30:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Mumzinda wa Tahapanesi mudzagwa mdima masana ndikadzathyola magoli a Iguputo kumeneko.+ Mphamvu zimene amanyadira zidzatha.+ Mitambo idzamuphimba ndipo anthu amʼmatauni ake adzatengedwa kupita ku ukapolo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena