Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 7:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ana aamuna akutola nkhuni, abambo akuyatsa moto ndipo akazi awo akukanda ufa kuti apange makeke okapereka nsembe kwa ‘Mfumukazi Yakumwamba.’*+ Ndipo akuthira pansi nsembe zachakumwa kwa milungu ina kuti andikhumudwitse.+

  • Yeremiya 44:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndiyeno amuna onse amene ankadziwa kuti akazi awo ankapereka nsembe kwa milungu ina, akazi onse amene anaimirira nʼkupanga gulu lalikulu komanso anthu onse amene ankakhala ku Iguputo+ mʼdera la Patirosi,+ anayankha Yeremiya kuti:

  • Yeremiya 44:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mʼmalomwake tichitadi zonse zimene tanena. Tipereka nsembe komanso tithira nsembe zachakumwa kwa Mfumukazi Yakumwamba.*+ Tichita zimenezi mofanana ndi mmene ife, makolo athu, mafumu athu ndi akalonga athu anachitira mʼmizinda ya Yuda ndi mʼmisewu ya Yerusalemu pamene tinkadya mkate nʼkukhuta ndipo zinthu zinkatiyendera bwino, moti sitinaone tsoka lililonse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena