Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 12:28, 29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Mfumuyo itakambirana ndi anthu ena inapanga ana awiri a ngʼombe agolide,+ kenako inauza anthu onse kuti: “Ndikuona kuti mukuvutika kwambiri kupita ku Yerusalemu. Ndiye ndakupangirani Mulungu uyu, amene anakutulutsani mʼdziko la Iguputo+ Aisiraeli inu.” 29 Choncho mwana wa ngʼombe wina anamuika ku Beteli+ ndipo wina anakamuika ku Dani.+

  • Hoseya 10:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Inu anthu a ku Beteli, wina adzakuchitaninso zimenezi+ chifukwa ndinu oipa kwambiri.

      Ndithu, mfumu ya Isiraeli idzawonongedwa* mʼbandakucha.”+

  • Amosi 5:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Musakhale ndi mtima wofuna kupita ku Beteli.+

      Ndipo musapite ku Giligala+ kapena ku Beere-seba.+

      Chifukwa ndithu Giligala adzapita ku ukapolo.+

      Ndipo Beteli adzawonongedwa.*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena