Numeri 21:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Tsoka iwe Mowabu! Mudzawonongedwa, inu anthu a Kemosi!+ Iye adzapangitsa ana ake aamuna kukhala othawa kwawo, ndipo adzasandutsa ana ake aakazi kukhala akapolo a Sihoni, mfumu ya Aamori. 1 Mafumu 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa nthawiyi mʼpamene Solomo anamangira Kemosi malo okwezeka.+ Kemosi anali mulungu wonyansa wa Amowabu ndipo anamʼmangira malowo paphiri lomwe linali pafupi ndi Yerusalemu. Anamangiranso Moleki,+ mulungu wonyansa wa Aamoni,+ malo okwezeka.
29 Tsoka iwe Mowabu! Mudzawonongedwa, inu anthu a Kemosi!+ Iye adzapangitsa ana ake aamuna kukhala othawa kwawo, ndipo adzasandutsa ana ake aakazi kukhala akapolo a Sihoni, mfumu ya Aamori.
7 Pa nthawiyi mʼpamene Solomo anamangira Kemosi malo okwezeka.+ Kemosi anali mulungu wonyansa wa Amowabu ndipo anamʼmangira malowo paphiri lomwe linali pafupi ndi Yerusalemu. Anamangiranso Moleki,+ mulungu wonyansa wa Aamoni,+ malo okwezeka.