Amosi 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova wanena kuti,‘“Chifukwa chakuti Aamoni andigalukira mobwerezabwereza,+ sindidzawasinthira chigamulo changa.Chifukwa anatumbula akazi apakati a ku Giliyadi kuti akulitse malo awo okhala.+ Amosi 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo mfumu yawo limodzi ndi akalonga ake adzapita ku ukapolo,”+ watero Yehova.’”
13 Yehova wanena kuti,‘“Chifukwa chakuti Aamoni andigalukira mobwerezabwereza,+ sindidzawasinthira chigamulo changa.Chifukwa anatumbula akazi apakati a ku Giliyadi kuti akulitse malo awo okhala.+