-
Malaki 1:3, 4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 “Esau ndinadana naye.+ Mapiri ake ndinawasandutsa bwinja+ ndipo cholowa chake ndinachisandutsa malo okhala mimbulu yamʼchipululu.”+
4 “Ngakhale kuti Edomu akunena kuti, ‘Ife tawonongedwa, koma tibwerera nʼkukamanga malo athu owonongedwawo,’ Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Iwo apita kukamanga, koma ine ndikagwetsa. Anthu adzatchula malo awowo kuti “dera la zoipa” ndipo iwowo adzatchedwa “anthu okanidwa ndi Yehova mpaka kalekale.”+
-