-
Yeremiya 25:27, 28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 “Ndiyeno ukawauze kuti, ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Imwani ndipo muledzere, musanze ndi kugwa osadzukanso+ chifukwa cha lupanga limene ndikutumiza pakati panu.”’ 28 Ngati angakakane kulandira kapuyi mʼmanja mwako kuti amwe, ukawauze kuti, ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Mukuyenera kumwa basi.
-