Yesaya 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Uwu ndi uthenga wokhudza Damasiko:+ “Taonani! Damasiko sadzakhalanso mzinda,Adzawonongedwa nʼkukhala mabwinja okhaokha.+ Amosi 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Yehova wanena kuti,‘“Popeza Damasiko anandigalukira mobwerezabwereza,* sindidzamusinthira chigamulo changa.Chifukwa anapuntha Giliyadi ndi zida zopunthira zachitsulo.+
17 Uwu ndi uthenga wokhudza Damasiko:+ “Taonani! Damasiko sadzakhalanso mzinda,Adzawonongedwa nʼkukhala mabwinja okhaokha.+
3 “Yehova wanena kuti,‘“Popeza Damasiko anandigalukira mobwerezabwereza,* sindidzamusinthira chigamulo changa.Chifukwa anapuntha Giliyadi ndi zida zopunthira zachitsulo.+