2 Mafumu 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mʼchaka cha 9 cha Hoshiya, mfumu ya Asuri inalanda Samariya+ nʼkutenga Aisiraeli kupita nawo ku Asuri.+ Mfumuyo inakaika Aisiraeliwo ku Hala ndi ku Habori pafupi ndi mtsinje wa Gozani+ ndiponso mʼmizinda ya Amedi.+ Yesaya 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova adzawabweretseramadzi ambiri komanso amphamvu a mu Mtsinje*Omwe ndi mfumu ya Asuri+ ndi ulemerero wake wonse. Mfumuyo idzadzaza timitsinje take tonseNʼkusefukira mʼmphepete mwake monse
6 Mʼchaka cha 9 cha Hoshiya, mfumu ya Asuri inalanda Samariya+ nʼkutenga Aisiraeli kupita nawo ku Asuri.+ Mfumuyo inakaika Aisiraeliwo ku Hala ndi ku Habori pafupi ndi mtsinje wa Gozani+ ndiponso mʼmizinda ya Amedi.+
7 Yehova adzawabweretseramadzi ambiri komanso amphamvu a mu Mtsinje*Omwe ndi mfumu ya Asuri+ ndi ulemerero wake wonse. Mfumuyo idzadzaza timitsinje take tonseNʼkusefukira mʼmphepete mwake monse