Mika 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndidzapirira mkwiyo wa Yehova,Chifukwa ndamuchimwira.+Ndidzaupirira mpaka ataweruza mlandu wanga nʼkundichitira chilungamo. Iye adzandipititsa pamalo owala,Ndipo ndidzaona chilungamo chake.
9 Ndidzapirira mkwiyo wa Yehova,Chifukwa ndamuchimwira.+Ndidzaupirira mpaka ataweruza mlandu wanga nʼkundichitira chilungamo. Iye adzandipititsa pamalo owala,Ndipo ndidzaona chilungamo chake.