Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 24:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma mofanana ndi nkhuyu zoipa zija, zimene ndi zoipa kwambiri moti munthu sangathe kudya,+ Yehova wanena kuti: “Ndi mmenenso ndidzaonere Zedekiya+ mfumu ya Yuda, akalonga ake, anthu onse opulumuka mu Yerusalemu amene atsalira mʼdzikoli komanso anthu okhala mʼdziko la Iguputo.+

  • Yeremiya 34:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndipo Mfumu Zedekiya ya Yuda ndi akalonga ake ndidzawapereka mʼmanja mwa adani awo, mʼmanja mwa anthu amene akufuna moyo wawo ndiponso mʼmanja mwa asilikali a mfumu ya ku Babulo+ amene akubwerera osamenyana nanu.’+

  • Yeremiya 37:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Kenako Mfumu Zedekiya inatuma anthu kuti akatenge Yeremiya.+ Atabwera naye, mfumuyo inamufunsa mafunso mwachinsinsi mʼnyumba mwake. Mfumuyo inamufunsa kuti: “Kodi pali mawu aliwonse ochokera kwa Yehova?” Yeremiya anayankha kuti: “Eya alipo!” Ndipo anapitiriza kuti: “Inuyo mudzaperekedwa mʼmanja mwa mfumu ya Babulo!”+

  • Yeremiya 38:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Koma ngati simudzadzipereka mʼmanja mwa akalonga* a mfumu ya Babulo, mzindawu udzaperekedwa mʼmanja mwa Akasidi ndipo adzauwotcha ndi moto.+ Inuyo simudzathawa mʼmanja mwawo.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena