1 Mafumu 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anaumba zipilala ziwiri zakopa.+ Chipilala chilichonse chinali chachitali mikono 18, ndipo kuzungulira chipilala chilichonse inali mikono 12.+ 1 Mafumu 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno Hiramu anaika zipilala zija pakhonde la kachisi.*+ Chipilala chimodzi anachiika mbali yakumanja* nʼkuchipatsa dzina lakuti Yakini.* Chipilala china anachiika mbali yakumanzere* nʼkuchipatsa dzina lakuti Boazi.*+
15 Anaumba zipilala ziwiri zakopa.+ Chipilala chilichonse chinali chachitali mikono 18, ndipo kuzungulira chipilala chilichonse inali mikono 12.+
21 Ndiyeno Hiramu anaika zipilala zija pakhonde la kachisi.*+ Chipilala chimodzi anachiika mbali yakumanja* nʼkuchipatsa dzina lakuti Yakini.* Chipilala china anachiika mbali yakumanzere* nʼkuchipatsa dzina lakuti Boazi.*+