1 Mbiri 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Azariya anabereka Seraya+ ndipo Seraya anabereka Yehozadaki.+ Ezara 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zimenezi zitachitika, mu ulamuliro wa mfumu Aritasasita+ ya ku Perisiya, Ezara*+ anabwera ku Yerusalemu kuchokera ku Babulo. Iye anali mwana wa Seraya.+ Seraya anali mwana wa Azariya, Azariya anali mwana wa Hilikiya,+
7 Zimenezi zitachitika, mu ulamuliro wa mfumu Aritasasita+ ya ku Perisiya, Ezara*+ anabwera ku Yerusalemu kuchokera ku Babulo. Iye anali mwana wa Seraya.+ Seraya anali mwana wa Azariya, Azariya anali mwana wa Hilikiya,+