Ekisodo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano mukadzamvera mawu anga mosamala ndi kusunga pangano langa, mudzakhaladi chuma changa chapadera pa anthu onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+ Yesaya 47:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ine ndinakwiyira anthu anga.+ Ndinalola kuti cholowa changa chidetsedwe+Ndipo ndinawapereka mʼmanja mwako.+ Koma iwe sunawachitire chifundo.+ Ngakhale munthu wokalamba unamusenzetsa goli lolemera kwambiri.+
5 Tsopano mukadzamvera mawu anga mosamala ndi kusunga pangano langa, mudzakhaladi chuma changa chapadera pa anthu onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+
6 Ine ndinakwiyira anthu anga.+ Ndinalola kuti cholowa changa chidetsedwe+Ndipo ndinawapereka mʼmanja mwako.+ Koma iwe sunawachitire chifundo.+ Ngakhale munthu wokalamba unamusenzetsa goli lolemera kwambiri.+