Yeremiya 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yerusalemu ndidzamusandutsa milu ya miyala+ ndiponso malo obisalamo mimbulu,+Ndipo mizinda ya Yuda ndidzaisandutsa mabwinja, popanda wokhalamo.+ Yeremiya 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tamvetserani, mdani akubwera! Kukumveka kugunda kwakukulu kuchokera kudziko lakumpoto,+Kumene kudzasandutsa mizinda ya Yuda kukhala mabwinja, malo obisalamo mimbulu.+
11 Yerusalemu ndidzamusandutsa milu ya miyala+ ndiponso malo obisalamo mimbulu,+Ndipo mizinda ya Yuda ndidzaisandutsa mabwinja, popanda wokhalamo.+
22 Tamvetserani, mdani akubwera! Kukumveka kugunda kwakukulu kuchokera kudziko lakumpoto,+Kumene kudzasandutsa mizinda ya Yuda kukhala mabwinja, malo obisalamo mimbulu.+