Yeremiya 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho Yehova wanena kuti: “Tsopano ndikuikira anthu awa zinthu zopunthwitsa,Ndipo iwo adzapunthwa ndi zinthu zimenezi,Abambo limodzi ndi ana,Munthu ndi mnzake woyandikana naye,Onse adzawonongedwa.”+ Ezekieli 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho azibambo amene ali mumzindawo adzadya ana awo+ ndipo ana adzadya abambo awo. Ine ndidzakulanga ndipo anthu ako onse otsala ndidzawabalalitsira kumbali zonse.”’+
21 Choncho Yehova wanena kuti: “Tsopano ndikuikira anthu awa zinthu zopunthwitsa,Ndipo iwo adzapunthwa ndi zinthu zimenezi,Abambo limodzi ndi ana,Munthu ndi mnzake woyandikana naye,Onse adzawonongedwa.”+
10 Choncho azibambo amene ali mumzindawo adzadya ana awo+ ndipo ana adzadya abambo awo. Ine ndidzakulanga ndipo anthu ako onse otsala ndidzawabalalitsira kumbali zonse.”’+