37 ine ndikusonkhanitsa pamodzi zibwenzi zako zonse zimene unkazisangalatsa, onse amene unkawakonda limodzi ndi onse amene unkadana nawo. Ndidzawasonkhanitsa pamodzi kuchokera kumadera onse ozungulira kuti akuukire ndipo ndidzakuvula kuti aone maliseche ako, moti adzakuona uli mbulanda.+