Oweruza 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho Aisiraeli anayamba kuchita zoipa pamaso pa Yehova ndipo anaiwala Yehova Mulungu wawo. Iwo ankalambiranso Abaala+ ndi mizati yopatulika.*+ 2 Mbiri 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo anasiya nyumba ya Yehova Mulungu wa makolo awo nʼkuyamba kutumikira mizati yopatulika* ndiponso mafano. Choncho Mulungu anakwiyira kwambiri Yuda ndi Yerusalemu chifukwa cha kulakwa kwawoko. 2 Mbiri 33:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Manase+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 12 ndipo analamulira zaka 55 ku Yerusalemu.+ 2 Mbiri 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye anamanganso malo okwezeka amene Hezekiya bambo ake anagwetsa.+ Anamanga maguwa ansembe a Abaala komanso mizati yopatulika,* ndipo ankagwadira gulu lonse la zinthu zakumwamba ndiponso kuzitumikira.+
7 Choncho Aisiraeli anayamba kuchita zoipa pamaso pa Yehova ndipo anaiwala Yehova Mulungu wawo. Iwo ankalambiranso Abaala+ ndi mizati yopatulika.*+
18 Iwo anasiya nyumba ya Yehova Mulungu wa makolo awo nʼkuyamba kutumikira mizati yopatulika* ndiponso mafano. Choncho Mulungu anakwiyira kwambiri Yuda ndi Yerusalemu chifukwa cha kulakwa kwawoko.
3 Iye anamanganso malo okwezeka amene Hezekiya bambo ake anagwetsa.+ Anamanga maguwa ansembe a Abaala komanso mizati yopatulika,* ndipo ankagwadira gulu lonse la zinthu zakumwamba ndiponso kuzitumikira.+