Deuteronomo 28:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Yehova adzakutumizirani adani anu kuti akuukireni ndipo mudzawatumikira+ muli ndi njala,+ ludzu, usiwa ndiponso mukusowa chilichonse. Iye adzakuvekani goli lachitsulo mʼkhosi lanu mpaka atakuwonongani. Yeremiya 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho ndidzakuchotsani mʼdziko lino nʼkukupititsani kudziko limene inu kapena makolo anu sankalidziwa.+ Kumeneko mukatumikira milungu ina masana ndi usiku+ chifukwa sindidzakuchitirani chifundo.”’
48 Yehova adzakutumizirani adani anu kuti akuukireni ndipo mudzawatumikira+ muli ndi njala,+ ludzu, usiwa ndiponso mukusowa chilichonse. Iye adzakuvekani goli lachitsulo mʼkhosi lanu mpaka atakuwonongani.
13 Choncho ndidzakuchotsani mʼdziko lino nʼkukupititsani kudziko limene inu kapena makolo anu sankalidziwa.+ Kumeneko mukatumikira milungu ina masana ndi usiku+ chifukwa sindidzakuchitirani chifundo.”’