Salimo 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye adzakhala ngati mtengo wodzalidwa mʼmbali mwa ngalande za madzi,Umene umabereka zipatso mʼnyengo yake,Umenenso masamba ake safota. Ndipo zonse zimene amachita zimamuyendera bwino.+ Salimo 92:12, 13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma olungama zinthu zidzawayendera bwino ngati mtengo wa kanjedzaNdipo adzakula kwambiri ngati mtengo wa mkungudza wa ku Lebanoni.+ 13 Iwo anadzalidwa mʼnyumba ya Yehova,Zinthu zikuwayendera bwino mʼmabwalo a Mulungu wathu.+
3 Iye adzakhala ngati mtengo wodzalidwa mʼmbali mwa ngalande za madzi,Umene umabereka zipatso mʼnyengo yake,Umenenso masamba ake safota. Ndipo zonse zimene amachita zimamuyendera bwino.+
12 Koma olungama zinthu zidzawayendera bwino ngati mtengo wa kanjedzaNdipo adzakula kwambiri ngati mtengo wa mkungudza wa ku Lebanoni.+ 13 Iwo anadzalidwa mʼnyumba ya Yehova,Zinthu zikuwayendera bwino mʼmabwalo a Mulungu wathu.+