Aroma 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzaweruza aliyense mogwirizana ndi zochita zake.+ Agalatiya 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musadzinamize, Mulungu sapusitsika. Chilichonse chimene munthu wafesa, adzakololanso chomwecho.+ Chivumbulutso 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ana ake ndidzawapha ndi mliri woopsa, moti mipingo yonse idzadziwa kuti ine ndi amene ndimafufuza maganizo* komanso mitima, ndipo aliyense payekha ndidzamubwezera mogwirizana ndi ntchito zake.+ Chivumbulutso 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ‘Taonani! Ndikubwera mofulumira ndipo ndili ndi mphoto yoti ndipereke kwa aliyense mogwirizana ndi ntchito yake.+
23 Ana ake ndidzawapha ndi mliri woopsa, moti mipingo yonse idzadziwa kuti ine ndi amene ndimafufuza maganizo* komanso mitima, ndipo aliyense payekha ndidzamubwezera mogwirizana ndi ntchito zake.+
12 ‘Taonani! Ndikubwera mofulumira ndipo ndili ndi mphoto yoti ndipereke kwa aliyense mogwirizana ndi ntchito yake.+