Salimo 73:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndithudi, anthu amene ali kutali ndi inu adzatheratu. Mudzawononga* aliyense amene akukusiyani pochita chigololo.*+ Yesaya 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Anthu opanduka ndi ochimwa adzawonongedwa limodzi,+Ndipo amene akusiya Yehova adzatha.+
27 Ndithudi, anthu amene ali kutali ndi inu adzatheratu. Mudzawononga* aliyense amene akukusiyani pochita chigololo.*+