Yeremiya 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Ndakuchititsa kuti ukhale ngati mpanda wakopa wolimba kwambiri kwa anthu awa.+ Iwo adzamenyana nawe ndithu,Koma sadzakugonjetsa,+Chifukwa ine ndili ndi iwe kuti ndikupulumutse komanso kukulanditsa,” akutero Yehova.
20 “Ndakuchititsa kuti ukhale ngati mpanda wakopa wolimba kwambiri kwa anthu awa.+ Iwo adzamenyana nawe ndithu,Koma sadzakugonjetsa,+Chifukwa ine ndili ndi iwe kuti ndikupulumutse komanso kukulanditsa,” akutero Yehova.