Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 5:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Tsoka kwa amene amanena kuti: “Agwire ntchito yake mofulumira.

      Ibwere mwamsanga kuti tiione.

      Cholinga* cha Woyera wa Isiraeli chichitike

      Kuti tichidziwe.”+

  • 2 Petulo 3:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 azidzati: “Kodi kukhalapo* kwake kolonjezedwa kuja kuli kuti?+ Taonani, palibe chimene chasintha kungochokera tsiku limene makolo athu anamwalira. Zinthu zonse zikupitiriza kuchitika ndendende ngati mmene zakhala zikuchitikira kuyambira pachiyambi cha chilengedwe.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena