-
Yeremiya 7:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 “Ukaime pageti la nyumba ya Yehova ndipo ukalengeze uthenga uwu, ‘Tamverani mawu a Yehova inu anthu nonse a mu Yuda, amene mumalowa pamageti awa kuti mukalambire Yehova.
-