Ezara 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo anamanga guwa lansembe pamalo ake akale ngakhale kuti ankaopa anthu a mitundu ina yowazungulira.+ Atatero anayamba kuperekerapo nsembe zopsereza kwa Yehova, zamʼmawa ndi zamadzulo.+
3 Iwo anamanga guwa lansembe pamalo ake akale ngakhale kuti ankaopa anthu a mitundu ina yowazungulira.+ Atatero anayamba kuperekerapo nsembe zopsereza kwa Yehova, zamʼmawa ndi zamadzulo.+