Salimo 79:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 79 Inu Mulungu, anthu a mitundu ina alowa mʼdziko limene ndi cholowa chanu.+Aipitsa kachisi wanu woyera.+Yerusalemu amusandutsa bwinja.+ Yeremiya 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yerusalemu ndidzamusandutsa milu ya miyala+ ndiponso malo obisalamo mimbulu,+Ndipo mizinda ya Yuda ndidzaisandutsa mabwinja, popanda wokhalamo.+
79 Inu Mulungu, anthu a mitundu ina alowa mʼdziko limene ndi cholowa chanu.+Aipitsa kachisi wanu woyera.+Yerusalemu amusandutsa bwinja.+
11 Yerusalemu ndidzamusandutsa milu ya miyala+ ndiponso malo obisalamo mimbulu,+Ndipo mizinda ya Yuda ndidzaisandutsa mabwinja, popanda wokhalamo.+