Mika 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho chifukwa cha anthu inu,Ziyoni adzalimidwa ngati munda,Yerusalemu adzakhala mabwinja.+Ndipo phiri la nyumba* ya Mulungu lidzakhala ngati zitunda zamunkhalango.+
12 Choncho chifukwa cha anthu inu,Ziyoni adzalimidwa ngati munda,Yerusalemu adzakhala mabwinja.+Ndipo phiri la nyumba* ya Mulungu lidzakhala ngati zitunda zamunkhalango.+