-
Yeremiya 36:11, 12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Mikaya mwana wa Gemariya, mwana wa Safani, atamva mawu onse a Yehova amene anali mumpukutumo, 12 anapita kunyumba ya mfumu, kuchipinda cha mlembi. Akalonga onse anali atakhala* pansi kumeneko ndipo kunali Elisama+ mlembi, Delaya mwana wa Semaya, Elinatani+ mwana wa Akibori,+ Gemariya mwana wa Safani, Zedekiya mwana wa Hananiya ndi akalonga ena onse.
-