Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 24:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Dzikolo laipitsidwa ndi anthu okhalamo,+

      Chifukwa anyalanyalaza malamulo,+

      Asintha malamulo+

      Ndipo aphwanya pangano limene linayenera kukhalapo mpaka kalekale.*+

  • Yeremiya 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Kenako ndinakulowetsani mʼdziko la minda ya zipatso,

      Kuti mudye zipatso zake ndi zinthu zabwino zamʼdzikolo.+

      Koma inu munalowa mʼdziko langa nʼkuliipitsa.

      Cholowa changa munachisandutsa chinthu chonyansa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena