2 Mafumu 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehoyakini+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 18 ndipo analamulira miyezi itatu ku Yerusalemu.+ Mayi ake anali a ku Yerusalemu ndipo dzina lawo linali Nehusita mwana wa Elinatani. Yeremiya 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 ‘Pali ine, Mulungu wamoyo,’ akutero Yehova, ‘ngakhale iwe Koniya*+ mwana wa Yehoyakimu,+ mfumu ya Yuda, utakhala mphete yodindira kudzanja langa lamanja, ndingakuvule!
8 Yehoyakini+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 18 ndipo analamulira miyezi itatu ku Yerusalemu.+ Mayi ake anali a ku Yerusalemu ndipo dzina lawo linali Nehusita mwana wa Elinatani.
24 ‘Pali ine, Mulungu wamoyo,’ akutero Yehova, ‘ngakhale iwe Koniya*+ mwana wa Yehoyakimu,+ mfumu ya Yuda, utakhala mphete yodindira kudzanja langa lamanja, ndingakuvule!