-
Yeremiya 24:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Dengu limodzi linali ndi nkhuyu zabwino kwambiri ngati nkhuyu zoyambirira kucha. Koma dengu lina linali ndi nkhuyu zoipa kwambiri. Zinali zoipa kwambiri moti munthu sakanatha kuzidya.
-