Yeremiya 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma inu munapitiriza kuchita zinthu zonsezi,’ akutero Yehova, ‘ndipo ngakhale kuti ndinkalankhula nanu mobwerezabwereza,* inu simunamvere.+ Ndinapitiriza kukuitanani koma inu simunayankhe.+
13 Koma inu munapitiriza kuchita zinthu zonsezi,’ akutero Yehova, ‘ndipo ngakhale kuti ndinkalankhula nanu mobwerezabwereza,* inu simunamvere.+ Ndinapitiriza kukuitanani koma inu simunayankhe.+