Yeremiya 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chifukwa maso anga akuona chilichonse chimene akuchita.* Anthuwo sanabisike kwa ine,Ndipo zolakwa zawo sizinabisike pamaso panga. Yeremiya 23:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Kodi pali munthu amene angabisale pamalo obisika amene ine sindingamuone?”+ akutero Yehova. “Kodi kumwamba kapena padziko lapansi, pali chilichonse chimene sindingachione?”+ akutero Yehova.
17 Chifukwa maso anga akuona chilichonse chimene akuchita.* Anthuwo sanabisike kwa ine,Ndipo zolakwa zawo sizinabisike pamaso panga.
24 “Kodi pali munthu amene angabisale pamalo obisika amene ine sindingamuone?”+ akutero Yehova. “Kodi kumwamba kapena padziko lapansi, pali chilichonse chimene sindingachione?”+ akutero Yehova.