Yeremiya 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako Pasuri anamenya mneneri Yeremiya n‘kumuika mʼmatangadza+ amene anali pa Geti Lakumtunda la Benjamini, limene linali mʼnyumba ya Yehova.
2 Kenako Pasuri anamenya mneneri Yeremiya n‘kumuika mʼmatangadza+ amene anali pa Geti Lakumtunda la Benjamini, limene linali mʼnyumba ya Yehova.