Yeremiya 33:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu a mu Yuda ndi a mu Isiraeli amene anatengedwa kupita kudziko lina ndidzawabwezeretsa+ ndipo adzakhalanso ngati mmene analili poyamba.+ Amosi 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 ‘Pa tsiku limenelo, ndidzadzutsa nyumba* ya Davide+ imene inagwa,Ndi kukonza malo amene khoma lake linawonongeka.Ndidzaikonza kuti isakhalenso bwinja.Ndipo ndidzaimanga kuti ikhale ngati mmene inalili kale.+
7 Anthu a mu Yuda ndi a mu Isiraeli amene anatengedwa kupita kudziko lina ndidzawabwezeretsa+ ndipo adzakhalanso ngati mmene analili poyamba.+
11 ‘Pa tsiku limenelo, ndidzadzutsa nyumba* ya Davide+ imene inagwa,Ndi kukonza malo amene khoma lake linawonongeka.Ndidzaikonza kuti isakhalenso bwinja.Ndipo ndidzaimanga kuti ikhale ngati mmene inalili kale.+