Deuteronomo 30:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ngakhale anthu a mtundu wanu amene anabalalitsidwawo atadzakhala kumalekezero kwa thambo, Yehova Mulungu wanu adzakusonkhanitsani nʼkukubweretsani kuchokera kumeneko.+ Ezekieli 20:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndidzakuchotsani pakati pa mitundu ya anthu ndipo ndidzakusonkhanitsani pamodzi kuchokera kumayiko amene munabalalikirako. Ndidzakusonkhanitsani ndi dzanja lamphamvu, mkono wotambasula ndi mkwiyo wosefukira.+ Ezekieli 34:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndidzasamalira nkhosa zanga ngati mʼbusa amene wapeza nkhosa zake zimene zinabalalika ndipo akuzidyetsa.+ Ndidzazipulumutsa mʼmalo onse amene zinabalalikira pa tsiku la mitambo ndi mdima wandiweyani.+
4 Ngakhale anthu a mtundu wanu amene anabalalitsidwawo atadzakhala kumalekezero kwa thambo, Yehova Mulungu wanu adzakusonkhanitsani nʼkukubweretsani kuchokera kumeneko.+
34 Ndidzakuchotsani pakati pa mitundu ya anthu ndipo ndidzakusonkhanitsani pamodzi kuchokera kumayiko amene munabalalikirako. Ndidzakusonkhanitsani ndi dzanja lamphamvu, mkono wotambasula ndi mkwiyo wosefukira.+
12 Ndidzasamalira nkhosa zanga ngati mʼbusa amene wapeza nkhosa zake zimene zinabalalika ndipo akuzidyetsa.+ Ndidzazipulumutsa mʼmalo onse amene zinabalalikira pa tsiku la mitambo ndi mdima wandiweyani.+