Yeremiya 50:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Mʼmasiku amenewo ndiponso pa nthawi imeneyo anthu a ku Isiraeli komanso anthu a ku Yuda adzabwera limodzi,”+ akutero Yehova. “Iwo azidzayenda akulira+ ndipo onse pamodzi adzafunafuna Yehova Mulungu wawo.+
4 “Mʼmasiku amenewo ndiponso pa nthawi imeneyo anthu a ku Isiraeli komanso anthu a ku Yuda adzabwera limodzi,”+ akutero Yehova. “Iwo azidzayenda akulira+ ndipo onse pamodzi adzafunafuna Yehova Mulungu wawo.+