Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 23:4, 5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Wamkulu dzina lake anali Ohola,* wamngʼono anali Oholiba.* Akazi amenewa anakhala anga ndipo anabereka ana aamuna ndi aakazi. Ohola akuimira Samariya+ ndipo Oholiba akuimira Yerusalemu.

      5 Ohola anayamba kuchita uhule+ ngakhale kuti anali mkazi wanga. Ankalakalaka kugona ndi amuna amene ankamukonda kwambiri+ omwe ndi Asuri amene ankakhala moyandikana naye.+

  • Ezekieli 23:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Choncho ndinamʼpereka mʼmanja mwa anthu amene ankamukonda kwambiri, omwe ndi amuna amʼdziko la Asuri+ amene ankalakalaka kugona naye.

  • Hoseya 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Imbani mlandu mayi anu. Aimbeni mlandu.

      Chifukwa iwowo si mkazi wanga+ ndipo ine si mwamuna wawo.

      Mayi anuwo asiye uhule*

      Komanso asiye kuchita chigololo.*

  • Hoseya 9:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Zoipa zawo zonse zinachitikira ku Giligala,+ ndipo ndinadana nawo kumeneko.

      Chifukwa cha zochita zawo zoipa, ndidzawathamangitsa panyumba yanga.+

      Ndipo sindidzawakondanso.+

      Akalonga awo onse ndi amakani.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena